Luka 22:59 - Buku Lopatulika59 Ndipo patapita ngati ora limodzi, wina ananenetsa, kuti, Zoonadi, munthu uyunso anali naye, pakuti ndiye Mgalileya Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201459 Ndipo patapita ngati ora limodzi, wina ananenetsa, kuti, Zoonadi, munthu uyunso anali naye, pakuti ndiye Mgalileya Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa59 Patapita ngati ora limodzi, munthu winanso adanenetsa kuti, “Ndithudi akulu aŵanso anali naye, pakuti ndi a ku Galileya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero59 Patatha pafupifupi ora limodzi, munthu winanso anati, “Zoonadi, munthu uyu anali ndi Iye, pakuti ndi mu Galileya.” Onani mutuwo |