Luka 22:57 - Buku Lopatulika57 Koma anakana, nati, Mkaziwe, sindimdziwa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Koma anakana, nati, Mkaziwe, sindimdziwa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Koma Petro adakana, adati, “Mai iwe, sindimdziŵa ameneyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Koma Petro anakana nati, “Mtsikana, ine sindimudziwa ameneyu.” Onani mutuwo |