Luka 22:58 - Buku Lopatulika58 Ndipo popita kamphindi, anamuona wina, nati, Iwenso uli mmodzi wa awo. Koma Petro anati, Munthu iwe, sindine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201458 Ndipo popita kamphindi, anamuona wina, nati, Iwenso uli mmodzi wa awo. Koma Petro anati, Munthu iwe, sindine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa58 Patapita kanthaŵi pang'ono, munthu wina pomuwona adati, “Akulu inu, ndinunso mmodzi mwa iwo aja.” Koma Petro adati, “Munthu iwe, ai ndithu sindine.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero58 Patatha kanthawi pangʼono, wina wake anamuona ndipo anati, “Iwenso ndiwe mmodzi mwa iwo.” Petro anayankha kuti, “Munthu iwe, ayi sindine.” Onani mutuwo |