Luka 22:56 - Buku Lopatulika56 Ndipo mdzakazi anamuona iye alikukhala m'kuwala kwake kwa moto, nampenyetsa iye, nati, Munthu uyunso anali naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201456 Ndipo mdzakazi anamuona iye alikukhala m'kuwala kwake kwa moto, nampenyetsa iye, nati, Munthu uyunso anali naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa56 Mtsikana wina wantchito adamuwona atakhala nao pamotopo. Adamuyang'anitsitsa, nati, “Aŵansotu anali naye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero56 Mtsikana wantchito anamuona atakhala nawo pafupi ndi moto. Iye anamuyangʼanitsitsa ndipo anati, “Munthu uyu anali ndi Yesu.” Onani mutuwo |