Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 22:55 - Buku Lopatulika

55 Ndipo pamene adasonkha moto m'kati mwa bwalo, nakhala pansi pamodzi, Petro anakhala pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

55 Ndipo pamene adasonkha moto m'kati mwa bwalo, nakhala pansi pamodzi, Petro anakhala pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

55 Iwo adasonkha moto m'kati mwa bwalo la nyumbayo, nakhala pansi pamodzi. Petro nayenso adakakhala pakati pao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

55 Koma pamene anasonkha moto pakati pa bwalo la milandu, anakhala onse pansi ndipo Petro anakhalanso pansi.

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:55
14 Mawu Ofanana  

Wodala munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, kapena wosaimirira m'njira ya ochimwa, kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza.


Musandikoke kundichotsa pamodzi ndi oipa, ndi ochita zopanda pake; amene alankhula zamtendere ndi anansi ao, koma mumtima mwao muli choipa.


Ukayenda ndi anzeru udzakhala wanzeru: koma mnzao wa opusa adzaphwetekedwa.


Lekani, achibwana inu, nimukhale ndi moyo; nimuyende m'njira ya nzeru.


Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa;


Ndipo pokhala Iye m'chipsinjo mtima anapemphera kolimba koposa ndithu: ndi thukuta lake linakhala ngati madontho aakulu a mwazi alinkugwa pansi.


Ndipo mdzakazi anamuona iye alikukhala m'kuwala kwake kwa moto, nampenyetsa iye, nati, Munthu uyunso anali naye.


Musanyengedwe; mayanjano oipa aipsa makhalidwe okoma.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa