Luka 22:54 - Buku Lopatulika54 Ndipo pamenepo anamgwira Iye, napita naye, nalowa m'nyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petro anatsata kutali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Ndipo pamenepo anamgwira Iye, napita naye, nalowa m'nyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petro anatsata kutali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Anthu aja adamugwira Yesu, napita naye ku nyumba ya mkulu wa ansembe onse. Petro ankaŵatsatira chapatali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Pamenepo anamugwira Iye, napita naye ndipo anamutengera ku nyumba ya mkulu wa ansembe. Petro anamutsatira patali. Onani mutuwo |