Luka 22:51 - Buku Lopatulika51 Koma Yesu anayankha nati, Lolani kufikira kumene. Ndipo anakhudza khutu lake, namchiritsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Koma Yesu anayankha nati, Lolani kufikira kumene. Ndipo anakhudza khutu lake, namchiritsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Koma Yesu adati, “Basi, lekani zimenezi.” Atatero adakhudza khutu la munthuyo namchiritsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Koma Yesu anayankha kuti, “Zisachitikenso zimenezi!” Ndipo Iye anakhudza khutu la munthuyo ndi kumuchiritsa. Onani mutuwo |