Luka 22:50 - Buku Lopatulika50 Ndipo wina wa iwo anakantha kapolo wa mkulu wa ansembe, namdula khutu lake lamanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Ndipo wina wa iwo anakantha kapolo wa mkulu wa ansembe, namdula khutu lake lamanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Apo mmodzi mwa iwo adatemadi wantchito wa mkulu wa ansembe onse, mpaka kumusenga khutu la ku dzanja lamanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Ndipo mmodzi wa iwo anatema wantchito wamkulu wa ansembe, nadula khutu lake lamanja. Onani mutuwo |