Luka 22:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo iye anachoka, nalankhulana ndi ansembe aakulu ndi akazembe mompereka Iye kwa iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo iye anachoka, nalankhulana ndi ansembe aakulu ndi akazembe mompereka Iye kwa iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Yudasiyo adapita kukapangana ndi akulu a ansembe ndi atsogoleri a alonda a ku Nyumba ya Mulungu za njira yoti aperekere Yesu kwa iwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndipo Yudasi anapita kwa akulu a ansembe ndi akulu oyangʼanira Nyumba ya Mulungu ndi kukambirana nawo za mmene iye angaperekere Yesu. Onani mutuwo |