Luka 22:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anati kwa iwo, Mafumu a anthu a mitundu awachitira ufumu; ndipo iwo amene awachitira ulamuliro anenedwa, Ochitira zabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anati kwa iwo, Mafumu a anthu a mitundu awachitira ufumu; ndipo iwo amene awachitira ulamuliro anenedwa, Ochitira zabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Yesu adaŵauza kuti, “Pakati pa anthu akunja, mafumu amadyera anthu ao masuku pa mutu, ndipo amene amaŵaonetsa mphamvu zao, amatchedwa mfulu zopatsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Yesu anawawuza kuti, “Mafumu a anthu a mitundu ina amaonetsa mphamvu za ufumu wawo pa anthuwo; ndipo amene ali ndi ulamuliro, amapatsidwa dzina la kuti ‘Opindula.’ Onani mutuwo |