Luka 22:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo kunakhala kutsutsana mwa iwo, ndani wa iwo ayesedwe wamkulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo kunakhala kutsutsana mwa iwo, ndani wa iwo ayesedwe wamkulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono ophunzira aja adayamba kutsutsana kuti, “Kodi mwa ife amati wamkulu ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Komanso mkangano unabuka pakati pawo kuti ndani mwa iwo amene amaganiziridwa kukhala wamkulu. Onani mutuwo |