Luka 22:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo anayamba kufunsana mwa iwo okha, ndiye yani mwa iwo amene adzachita ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Apo onse adayamba kumafunsana kuti, “Kodi ndani mwa ife angachite zotere?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iwo anayamba kufunsana pakati pawo kuti ndi ndani wa iwo amene akanachita ichi. Onani mutuwo |