Luka 22:16 - Buku Lopatulika16 pakuti ndinena ndi inu, sindidzadya kufikira udzakwaniridwa mu Ufumu wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 pakuti ndinena ndi inu, sindidzadya kufikira udzakwaniridwa mu Ufumu wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pakuti kunena zoona, sindidzadyanso konse Paska, mpaka Paskayi itadzafika pake penipeni mu Ufumu wa Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakuti Ine ndikukuwuzani kuti sindidzadyanso Paska wina mpaka Paskayi itakwaniritsidwa mu ufumu wa Mulungu.” Onani mutuwo |