Luka 22:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo itadza nthawi yake, Iye anakhala pachakudya, ndi ophunzira pamodzi ndi Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo itadza nthawi yake, Iye anakhala pachakudya, ndi ophunzira pamodzi ndi Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Nthaŵi itakwana, Yesu adakakhala podyera pamodzi ndi atumwi ake aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ora litakwana, Yesu ndi ophunzira ake anakhala pa tebulo. Onani mutuwo |