Luka 22:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anapita iwo, napeza monga adatero nao; ndipo anakonza Paska. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anapita iwo, napeza monga adatero nao; ndipo anakonza Paska. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono iwo adapita nakachipezadi monga momwe adaaŵauzira, ndipo adakonza phwando la Paska. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iwo anapita nakapeza zinthu monga mmene Yesu anawawuzira. Tsono anakonza Paska. Onani mutuwo |