Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 22:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa chinayandikira, ndicho chotchedwa Paska.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo phwando la mikate yopanda chotupitsa linayandikira, ndilo lotchedwa Paska.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Nthaŵi yochitira chikondwerero cha buledi wosafufumitsa inkayandikira. Chikondwererocho chimatchedwa Paska.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Phwando la buledi wopanda yisiti lotchedwa Paska litayandikira,

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:1
9 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m'dziko la Ejipito, ndi kuti,


Ndipo tsiku loyamba la mikate yopanda chotupitsa, pamene amapha Paska, ophunzira ananena naye, Mufuna tinke kuti, tikakonze mkadyereko Paska?


Koma pasanafike chikondwerero la Paska, Yesu, podziwa kuti nthawi yake idadza yakuchoka kutuluka m'dziko lino lapansi, kunka kwa Atate, m'mene anakonda ake a Iye yekha a m'dziko lapansi, anawakonda kufikira chimaliziro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa