Luka 22:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anafunafuna maphedwe ake pakuti anaopa anthuwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anafunafuna maphedwe ake pakuti anaopa anthuwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Akulu a ansembe ndi aphunzitsi a Malamulo ankafunafuna njira yoti aphere Yesu. Paja iwo ankaopa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 akulu a ansembe ndi aphunzitsi amalamulo amafunafuna mpata woti amuphere Yesu, pakuti ankachita mantha ndi anthu. Onani mutuwo |