Luka 21:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo anthu onse analawira mamawa kudza kwa Iye ku Kachisi kudzamvera Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo anthu onse analawira mamawa kudza kwa Iye ku Kachisi kudzamvera Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Tsono anthu onse ankalaŵirira m'mamaŵa kubwera kwa Iye ku Nyumba ya Mulungu kudzamva mau ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Ndipo anthu onse amabwera mmamawa kudzamumva Iye ku Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwo |