Luka 21:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adaonanso mai wina wamasiye akuponyamo tindalama tiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anaonanso mkazi wamasiye wosauka akuyikamo timakopala tiwiri. Onani mutuwo |