Luka 21:14 - Buku Lopatulika14 Chifukwa chake tsimikizani mumtima mwanu, kuti usanafike mlandu musalingirire chimene mudzayankha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Chifukwa chake tsimikizani mumtima mwanu, kuti usanafike mlandu musalingirire chimene mudzayankha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono mudziŵiretu kuti musadzachite kukonzekera mau oti mudzaŵayankhe pamlandupo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Koma tsimikizani mtima kuti musadzade nkhawa za momwe mudzadzitchinjirizire. Onani mutuwo |