Luka 20:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anatsutsana mwa okha, nanena, Ngati tinena uchokera Kumwamba; adzati, Simunamkhulupirire chifukwa ninji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anatsutsana mwa okha, nanena, Ngati tinena uchokera Kumwamba; adzati, Simunamkhulupirira chifukwa ninji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwo aja adayamba kukambirana nkumati, “Tikati adaazitenga kwa Mulungu, Iyeyu anena kuti, ‘Nanga bwanji tsono sumudamkhulupirire?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo anakambirana pakati pawo ndikuti, “Ngati ife tinena kuti, ‘Kuchokera kumwamba’ Iye akatifunsa kuti, ‘chifukwa chiyani simunamukhulupirire iye?’ Onani mutuwo |