Luka 20:4 - Buku Lopatulika4 Ubatizo wa Yohane unachokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ubatizo wa Yohane unachokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 kodi Yohane Mbatizi kuti azibatiza, mphamvu zake adaazitenga kwa yani, kwa Mulungu kapena kwa anthu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ‘Kodi ubatizo wa Yohane, unali wochokera kumwamba, kapena wochokera kwa anthu?’ ” Onani mutuwo |