Luka 20:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Ndidzakufunsani mau Inenso; mundiuze: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Ndidzakufunsani mau Inenso; mundiuze: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yesu adati, “Nanenso ntakufunsani funso limodzi. Tandiwuzani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye anayankha kuti, “Inenso ndikufunsani, mundiyankhe, Onani mutuwo |