Luka 20:2 - Buku Lopatulika2 ndipo anati, nanena naye, Mutiuze muchita izi ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo anati, nanena naye, Mutiuze muchita izi ndi ulamuliro wotani? Kapena ndani iye amene anakupatsani ulamuliro umene? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 namufunsa kuti, “Mutiwuze, kodi mphamvu zoti muzichita zimenezi mudazitenga kuti? Kaya ndani adakupatsani mphamvu zimenezi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iwo anati, “Mutiwuze mukuchita izi ndi ulamuliro wayani? Ndani anakupatsani ulamuliro uwu?” Onani mutuwo |