Luka 20:6 - Buku Lopatulika6 Ndiponso, tikanena, Uchokera kwa anthu; anthu onse adzatiponya miyala: pakuti akopeka mtima, kuti Yohane ali mneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndiponso, tikanena, Uchokera kwa anthu; anthu onse adzatiponya miyala: pakuti akopeka mtima, kuti Yohane ali mneneri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Komanso tikati adaazitenga kwa anthu, anthu onseŵa atiponya miyala, chifukwa mumtima mwao amatsimikiza kuti Yohane adaali mneneri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma ngati ife tinena kuti, ‘kuchokera kwa anthu,’ anthu onse atigenda miyala, chifukwa amatsimikiza kuti Yohane anali mneneri.” Onani mutuwo |