Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 20:41 - Buku Lopatulika

41 Koma Iye anati kwa iwo, Amanena bwanji kuti Khristuyo ndiye mwana wa Davide?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Koma Iye anati kwa iwo, Amanena bwanji kuti Khristuyo ndiye mwana wa Davide?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Yesu adaŵafunsa kuti, “Kodi inu, bwanji amati Mpulumutsi wolonjezedwa uja ndi mwana wa Davide?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Kenaka Yesu anawawuza kuti, “Zikutheka bwanji kuti aziti Khristu ndi mwana wa Davide?

Onani mutuwo Koperani




Luka 20:41
14 Mawu Ofanana  

pamenepo pangano langa lidzasweka ndi Davide mtumiki wanga, kuti asakhale ndi mwana wamwamuna wakulamulira pa mpando wa ufumu wake; ndiponso ndi Alevi ansembe, atumiki anga.


Buku la kubadwa kwa Yesu Khristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu.


Ndipo popita Yesu kuchokera kumeneko, anamtsata Iye anthu awiri akhungu, ofuula ndi kuti, Mutichitire ife chifundo, mwana wa Davide.


Kodi sichinati chilembo kuti Khristu adza kutuluka mwa mbeu ya Davide, ndi kuchokera ku Betelehemu, kumudzi kumene kunali Davide?


Potero, pokhala mneneri iye, ndi kudziwa kuti ndi lumbiro anamlumbirira Mulungu, kuti mwa chipatso cha m'chuuno mwake adzakhazika wina pa mpando wachifumu wake;


Ine Yesu ndatuma mngelo wanga kukuchitirani umboni za izi mu Mipingo. Ine ndine muzu ndi mbadwa ya Davide, nyenyezi yonyezimira ya nthanda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa