Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 20:40 - Buku Lopatulika

40 Pakuti sanalimbenso mtima kumfunsa Iye kanthu kena.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Pakuti sanalimbenso mtima kumfunsa Iye kanthu kena.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Adaatero popeza kuti Asaduki aja sadalimbenso mtima kuti amufunse mafunso ena.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Ndipo panalibe wina amene akanalimba mtima kumufunsa Iye mafunso ena.

Onani mutuwo Koperani




Luka 20:40
5 Mawu Ofanana  

Yankha chitsiru monga mwa utsiru wake, kuti asadziyese wanzeru.


Ndipo sanalimbike mtima munthu aliyense kumfunsa kanthu kuyambira tsiku lomwelo.


Ndipo pakuona kuti anayankha ndi nzeru, Yesu anati kwa iye, Suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu. Ndipo palibe munthu analimbanso mtima kumfunsa Iye kanthu.


Ndipo iwo sanathe kumbwezera mau pa zinthu izi.


Ndipo alembi ena anayankha nati, Mphunzitsi, mwanena bwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa