Luka 20:18 - Buku Lopatulika18 Munthu yense wakugwa pamwala uwu, adzaphwanyika; koma iye amene udzamgwera, udzamupha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Munthu yense wakugwa pa mwala uwu, adzaphwanyika; koma iye amene udzamgwera, udzamupha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Aliyense wogwera pa mwala umenewo adzathyokathyoka. Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere, udzangomutswanyiratu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Aliyense amene agwa pa mwalawu adzapweteka, koma iye amene udzamugwera udzamuphwanya.’ ” Onani mutuwo |