Luka 20:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo alembi ndi ansembe aakulu anafunafuna kumgwira ndi manja nthawi yomweyo; ndipo anaopa anthu; pakuti anazindikira kuti ananenera pa iwo fanizo ili. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo alembi ndi ansembe aakulu anafunafuna kumgwira ndi manja nthawi yomweyo; ndipo anaopa anthu; pakuti anazindikira kuti ananenera pa iwo fanizo ili. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Aphunzitsi a Malamulo ndi akulu a ansembe adaadziŵa kuti fanizolo Yesu ankaphera iwowo. Nchifukwa chake ankafuna kumugwira nthaŵi yomweyo, koma ankaopa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Aphunzitsi amalamulo ndi akulu a ansembe amafuna njira yoti amuphe nthawi yomweyo, chifukwa anadziwa kuti ananena fanizo ili powatsutsa iwo. Koma iwo anali ndi mantha chifukwa cha anthu. Onani mutuwo |