Luka 20:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anatumizanso kapolo wina; ndipo iyenso anampanda, namchitira chipongwe, nambweza, wopanda kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anatumizanso kapolo wina; ndipo iyenso anampanda, namchitira chipongwe, nambweza, wopanda kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Adatumanso wantchito wina. Nayenso alimi aja adammenya, namchita chipongwe, nkumubweza osampatsa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye anatumiza wantchito wina, koma uyunso anamumenya namuchita zachipongwe ndi kumubweza wopanda kanthu. Onani mutuwo |