Luka 20:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anatumizanso wina wachitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anatumizanso wina wachitatu; ndipo iyenso anamlasa, namtaya kunja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adatumanso wachitatu, koma uyunso alimiwo adamuvulaza, namtaya kunja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anatumizanso wina wachitatu ndipo iwo anamuvulaza namuponya kunja. Onani mutuwo |