Luka 2:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo iwo, m'mene anaona, anadziwitsa anthu za mau analankhulidwa kwa iwo a mwana uyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo iwo, m'mene anaona, anadziwitsa anthu za mau analankhulidwa kwa iwo a mwana uyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamene adamuwona, abusawo adaŵafotokozera zimene mngelo uja adaaŵauza za mwanayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pamene anamuona Iye, iwo anafotokoza zomwe anawuzidwa za mwanayo, Onani mutuwo |