Luka 2:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo iwo anadza ndi changu, napeza Maria, ndi Yosefe, ndi mwana wakhanda atagona modyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo iwo anadza ndi changu, napeza Maria, ndi Yosefe, ndi mwana wakhanda atagona modyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono adapita mofulumira, nakapeza Maria ndi Yosefe, atagoneka mwana wakhandayo m'chodyera cha zoŵeta chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo iwo anafulumira nyamuka nakapeza Mariya ndi Yosefe ndi mwana wakhanda, amene anagona modyera ngʼombe. Onani mutuwo |