Luka 2:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ichi ndi chizindikiro kwa inu: Mudzapeza mwana wakhanda wokuta ndi nsalu atagona modyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ichi ndi chizindikiro kwa inu: Mudzapeza mwana wakhanda wokuta ndi nsalu atagona modyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Chitsimikizo chake ndi ichi: mukapeza mwana wakhanda, wokutidwa ndi nsalu, atagona m'chodyera cha zoŵeta.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ichi chidzakhala chizindikiro kwa inu: mukapeza mwana wakhanda wokutidwa ndi nsalu atagona modyera ngʼombe.” Onani mutuwo |