Luka 2:11 - Buku Lopatulika11 pakuti wakubadwirani inu lero, m'mzinda wa Davide, Mpulumutsi, amene ali Khristu Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 pakuti wakubadwirani inu lero, m'mudzi wa Davide, Mpulumutsi, amene ali Khristu Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Usiku womwe uno m'mudzi wa Davide wakubadwirani Mpulumutsi, amene ndi Khristu Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Lero mʼmudzi wa Davide wakubwadwirani Mpulumutsi; Iye ndi Khristu Ambuye. Onani mutuwo |