Luka 19:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo m'mene anachiona anadandaula onse, nanena, Analowa amchereze munthu ali wochimwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo m'mene anachiona anadandaula onse, nanena, Analowa amchereze munthu ali wochimwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Poona zimenezi, anthu onse adayamba kung'ung'udza. Adati, “Wakakhala kunyumba kwa munthu wochimwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Anthu onse ataona zimenezi anayamba kungʼungʼudza, nati, “Iye akupita kuti akakhale mlendo wa wochimwa.” Onani mutuwo |