Luka 19:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anafulumira, natsika, namlandira Iye wokondwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anafulumira, natsika, namlandira Iye wokondwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pompo Zakeyo adafulumira, natsika, kenaka nkukamlandiradi Yesu mokondwa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo nthawi yomweyo anatsika ndipo anamulandira mosangalala. Onani mutuwo |