Luka 19:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo m'mene anayandikira, anaona mzindawo naulirira, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo m'mene anayandikira, anaona mudziwo naulirira, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Yesu atayandikira, nkuwona Yerusalemu, adalira chifukwa cha mzindawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Iye atayandikira ku Yerusalemu ndi kuona mzindawo, anawulirira Onani mutuwo |