Luka 19:30 - Buku Lopatulika30 nati, Mukani kumudzi uli pandunji panu; m'menemo, polowa, mudzapeza mwana wa bulu womangidwa, pamenepo palibe munthu anakwerapo nthawi iliyonse; mummasule iye nimumtenge. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 nati, Mukani kumudzi uli pandunji panu; m'menemo, polowa, mudzapeza mwana wa bulu womangidwa, pamenepo palibe munthu anakwerapo nthawi iliyonse; mummasule iye nimumtenge. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 naŵauza kuti, “Pitani m'mudzi mukuwonawo. Mukakangoloŵamo mukapeza mwanawabulu ali chimangire, amene munthu sanakwerepo chikhalire. Mukammasule, nkubwera naye kuno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 “Pitani mʼmudzi uli patsogolo panu, mukakalowa mʼmudzimo, mukapeza mwana wabulu womangiriridwa amene wina aliyense sanakwerepo. Mukamumasule ndi kubwera naye kuno. Onani mutuwo |