Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 19:31 - Buku Lopatulika

31 Ndipo munthu akati kwa inu, Mummasuliranji? Mudzatero naye, Ambuye amfuna iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Ndipo munthu akati kwa inu, Mummasuliranji? Mudzatero naye, Ambuye amfuna iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Wina akakakufunsani kuti, ‘Mukummasuliranji?’ Mukati, ‘Ambuye ali naye ntchito.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Ngati wina aliyense akakufunsani kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mukumumasula mwana buluyo?’ Mukamuwuze kuti, ‘Ambuye akumufuna.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:31
7 Mawu Ofanana  

Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zake zomwe, dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.


nati, Mukani kumudzi uli pandunji panu; m'menemo, polowa, mudzapeza mwana wa bulu womangidwa, pamenepo palibe munthu anakwerapo nthawi iliyonse; mummasule iye nimumtenge.


Ndipo anachoka otumidwawo, napeza monga adanena kwa iwo.


Mau amene anatumiza kwa ana a Israele, akulalikira Uthenga Wabwino wa mtendere mwa Yesu Khristu (ndiye Ambuye wa onse)


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa