Luka 18:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo mkulu wina anamfunsa Iye, nanena, Mphunzitsi wabwino, ndizichita chiyani, kuti ndilowe moyo wosatha? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo mkulu wina anamfunsa Iye, nanena, Mphunzitsi wabwino, ndizichita chiyani, kuti ndilowe moyo wosatha? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mkulu wina adafunsa Yesu kuti, “Aphunzitsi abwino, kodi ndizichita chiyani kuti ndikalandire moyo wosatha?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Oweruza wina wake anamufunsa Iye kuti, “Aphunzitsi abwino, ndichite chiyani kuti ndilandire moyo wosatha?” Onani mutuwo |