Luka 18:17 - Buku Lopatulika17 Indetu ndinena kwa inu, Aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana, sadzalowamo ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Indetu ndinena kwa inu, Aliyense wosalandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana, sadzalowamo ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Ndithu ndikunenetsa kuti amene salandira Ufumu wa Mulungu ngati mwana, ameneyo sadzaloŵamo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti aliyense amene salandira ufumu wa Mulungu ngati mwana wamngʼono, sadzalowamo.” Onani mutuwo |