Luka 17:18 - Buku Lopatulika18 Akubwera kulemekeza Mulungu sanapezeke mmodzi kodi, koma mlendo uyu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Akubwera kulemekeza Mulungu sanapezeka mmodzi kodi, koma mlendo uyu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndiye kuti sadabwerere wina aliyense kudzayamika Mulungu, koma mlendo yekhayu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kodi palibe mmodzi mwa iwo amene anabwerera kudzalemekeza Mulungu kupatula mlendoyu?” Onani mutuwo |