Luka 17:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Yesu anayankha nati, Kodi sanakonzedwe khumi? Koma ali kuti asanu ndi anai aja? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Yesu anayankha nati, Kodi sanakonzedwe khumi? Koma ali kuti asanu ndi anai aja? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Apo Yesu adati, “Kodi achira aja si khumi? Nanga asanu ndi anai ena aja ali kuti? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Yesu anafunsa kuti, “Kodi amene anachiritsidwa sanalipo khumi? Nanga asanu ndi anayi ena ali kuti? Onani mutuwo |