Luka 17:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anati kwa iye, Nyamuka, nupite; chikhulupiriro chako chakupulumutsa iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anati kwa iye, Nyamuka, nupite; chikhulupiriro chako chakupulumutsa iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Kenaka Yesu adauza munthuyo kuti, “Nyamuka, pita. Chikhulupiriro chako chakuchiritsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Pamenepo anati kwa iye, “Imirira ndipo pita; chikhulupiriro chako chakuchiritsa iwe.” Onani mutuwo |