Luka 17:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo mmodzi wa iwo, pakuona kuti anachiritsidwa, anabwerera m'mbuyo, nalemekeza Mulungu ndi mau aakulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo mmodzi wa iwo, pakuona kuti anachiritsidwa, anabwerera m'mbuyo, nalemekeza Mulungu ndi mau akulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono mmodzi mwa iwo, ataona kuti wachira, adabwerera nayamba kuyamika Mulungu mokweza mau. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mmodzi wa iwo, ataona kuti wachiritsidwa, anabwerera, nayamika Mulungu ndi mawu okweza. Onani mutuwo |