Luka 16:7 - Buku Lopatulika7 Pomwepo anati kwa wina, Ndipo iwe uli nao mangawa otani? Ndipo uyu anati, Madengu a tirigu zana. Iye ananena naye, Tenga kalata yako nulembere makumi asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pomwepo anati kwa wina, Ndipo iwe uli nao mangawa otani? Ndipo uyu anati, Madengu a tirigu zana. Iye ananena naye, Tenga kalata wako nulembere makumi asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adafunsanso wina kuti, ‘Nanga iwe, ngongole yako ndi yotani?’ Iye adati, ‘Tirigu wamuyeso wokwanira matumba makumi khumi.’ Kapitaoyo adamuuza kuti, ‘Nayi kalata yako yangongole, ungolembapo matumba makumi asanu ndi atatu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Kenaka iye anafunsa wachiwiri kuti, ‘Nanga iwe uli ndi ngongole yotani?’ “Iye ayankha kuti madengu a tirigu 1,000. “Iye anati, ‘Tenga pamene unalemba ngongole yakoyo ndipo ulembepo 800.’ Onani mutuwo |