Luka 16:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anadziitanira mmodzi ndi mmodzi amangawa onse a mbuye wake, nanena kwa woyamba, Unakongola chiyani kwa mbuye wanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anadziitanira mmodzi ndi mmodzi amangawa onse a mbuye wake, nanena kwa woyamba, Unakongola chiyani kwa mbuye wanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Motero adaitana angongole a mbuye wake mmodzimmodzi. Adafunsa woyamba kuti, ‘Kodi uli ndi ngongole yotani kwa mbuye wanga?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “Choncho iye anayitana aliyense amene anali ndi ngongole kwa bwana wake. Iye anafunsa woyamba, ‘Kodi uli ndi ngongole yotani kwa bwana wanga?’ Onani mutuwo |