Luka 16:4 - Buku Lopatulika4 Ndidziwa chimene ndidzachita, kotero kuti pamene ananditulutsa muukapitao, anthu akandilandire kunyumba kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndidziwa chimene ndidzachita, kotero kuti pamene ananditulutsa muukapitao, anthu akandilandire kunyumba kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Chabwino, tsopano ndadziŵa choti ndichite, kuti anthu akandilandire ku nyumba zao, ukapitao ukandithera.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ine ndikudziwa chimene ndidzachita kotero kuti, pamene ntchito yanga yatha pano, anthu adzandilandire mʼnyumba zawo.’ Onani mutuwo |