Luka 16:11 - Buku Lopatulika11 Chifukwa chake ngati simunakhale okhulupirika m'chuma cha chosalungama, adzakhulupirira inu ndani ndi chuma choona? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Chifukwa chake ngati simunakhala okhulupirika m'chuma cha chosalungama, adzakhulupirira inu ndani ndi chuma choona? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono ngati mwakhala osakhulupirika pa chuma chonyengachi, ndani nanga adzakusungizeni chuma chenicheni? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo ngati simunakhale okhulupirika pogwiritsa ntchito chuma cha dziko lapansi, ndani amene adzakusungitsani chuma chenicheni? Onani mutuwo |